Kudzera m’nkhani ya mmene Mulungu anagwiritsira ntchito asilikali a Gideoni 300 kuti agonjetse adani 135,000 ndi nkhani ya mmene Yoswa adagonjetsa Yeriko pozungulira ndi kufuula, titha kuona kuti palikonse pomwe pali kumvera ku mawu a Mulungu, palinso zozizwa.
Pambuyo pa m’badwo wa Atate ndi Mwana, mu m’badwo uno wa Mzimu Woyera, iwo amene amatsatira mawu a Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, “Lalikirani Uthenga Wabwino kwa mitundu yonse. Khalani ogwirizana m’chikondi,” ndi mtima womvera, adzachitira umboni zozizwa.
Koma kolingana ndi kuuma kwako, ndi mtima wako wosalapa, ulikudziunjikira wekha mkwiyo pa tsiku la mkwiyo ndi la kuvumbulutsa kuweruza kolungama kwa Mulungu; Mulungu “adzabwezera munthu aliyense kolingana ndi ntchito zake.” Aroma 2:5–6
Ndipo ananena nao, Mukani kudziko lonse lapansi, lalikirani Uthenga Wabwino kwa olengedwa onse. Amene akhulupirira nabatizidwa, adzapulumutsidwa; koma amene sakhulupirira adzalangidwa. Marko 16:15-16
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi