Uthenga Wabwino wa Mpingo wa Mulungu, umene unayamba m’malo ang’onoang ‘ono ngati chipinda chapamwamba cha Marko, wakula pansi pa dalitso ndi chitsogozo cha Mulungu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai ndipo tsopano wakhala mpingo wapadziko lonse umene wafalitsa uthenga wabwino padziko lonse lapansi.
Ngati timasangalala ndi maganizo ndi moyo umene umatsutsana ndi chifuniro cha Mulungu, sitingathe kuchita bwino. Aisraele anachimwa ndi kukayikira mphamvu ya Mulungu ngakhale anaona zozizwitsa Zake zambiri, koma ngati timayamikira Mulungu amene nthawi zonse amatithandiza, tidzalandira madalitso ambiri.
Uzolowerane ndi Iye, nukhale ndi mtendere; ukatero zokoma zidzakudzera. Landira tsono chilamulo pakamwa pake, nuwasunge maneno ake mumtima mwako. Ukabweranso kwa Wamphamvuyonse, udzamanga bwino; ukachotsera chosalungama kutali kwa mahema ako. and assign your nuggets to the dust, your gold of Ophir to the rocks in the ravines, Ndipo utaye chuma chako kufumbi, ndi golide wa ku Ofiri ku miyala ya kumitsinje. Ndipo Wamphamvuyonse adzakhala chuma chako, ndi ndalama zako zofunika. Yobu 22:21-25
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi