Nali funso lina: Pamene Mulungu anaika mtengo wakudziwitsa zabwino ndi zoipa m’munda wa Edene, kodi anadziŵa kuti Adamu adzadya zipatso zake, kapena ayi?
Sitinganene kuti Mulungu Wamphamvuyonse, amene analengeza mapeto kuyambira pachiyambi, sanadziwe (Yes 46:10). Ngati Mulungu ankadziwa, ayenera kuti ankafuna kuti Adamu ndi Hava achimwe. Ngakhale njoka imene inayesa Hava inapangidwanso ndi Mulungu. Chinali chikhazikitso cha Mulungu kuti Adamu ndi Hava anyengedwe ndi njoka ndi kudya zipatso za mtengo wakudziwitsa zabwino ndi zoipa.
(Gen 3:1-5).
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi