M’dziko la angelo momwe mulibe malire mu liwiro, titha kuwona yunivesi yonse pafupifupi kwa ola limodzi. M’buku la Daniele, Danieli atangoyamba kupemphera 3 koloko masana [pafupifupi nthawi yopereka nsembe yamadzulo], mngelo Gabriele anabwera ndikumuuza uthenga wa Mulungu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi