Munthu amabadwa, koma sangathawe imfa. Munthu amabadwa ndi kufa, wina amabadwa kenako nkufa . . .
Kodi ndi anthu angati omwe anabadwa ndipo adamwalira kufikira lero? Ngakhale zimanenedwa kuti munthu ndi mbuye wa Chilengedwe chonse, iye ndikapolo chabe wa imfa.
Ndichifukwa chiyani mbuye wa chilengedwe chonse wakhala kapolo wa imfa?
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi