Anthu amene aphunzirapo kanthu pa ulendo wa zaka 40 wa Aisiraeli m’chipululu ndi kumvera Mulungu ndi chikhulupiriro m’lonjezo Lake adzadalitsidwa m’zonse zimene amachita, popanda kufafanizidwa m’buku la Mulungu.
Mu M’badwo wa Mzimu Woyera, Tiyenera Kudziwa Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi
Mulungu Yehova yemwe anapulumutsa Aisrayeli ku Igupto, ndi Yesu amene anakhululukira machimo a anthu kudzera m’mwazi Wake wamtengo wapatali wokhetsedwa pa mtanda, ndi Khristu Ahnsahnghong amene anabwezeretsa choonadi mu m’badwo uno ndi Mulungu mmodzi.
“Ndipo kudzali mukadzamvera mau a Yehova Mulungu wanu mwachangu, ndi kusamalira kuchita malamulo ake onse amene ndikuuzani lero kuti Yehova Mulungu wanu adzakukulitsani koposa amitundu onse a pa dziko lapansi.” Deuteronomo 28:1
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi