Tingapulumuke pokhapokha ngati tilandira Khristu amene wabwera pa mitambo chiweruzo cha moto chisanachitike. Kudzera mu ulosi ndi kukwaniritsidwa kwa Yesu, zikuonekeratu kuti mitambo si mitambo yeniyeni ya kumwamba koma ndi fanizo la m'Baibulo lophiphiritsira thupi.
Kubwera kwake kachiwiri m'thupi kunaloseredwa monga kubwera pa mitambo chifukwa monga mitambo imaphimba dzuwa, thupinso limaphimba ulemerero wa Mulungu, ndipo monga zinthu zonse zimatsitsimutsidwa ndi mvula ya m'mitambo, momwemonso Mulungu amabwera m'thupi kudzapulumutsa anthu ndi mawu a madzi amoyo.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi