Pamene Rute, mkazi wa ku Mowabu, anatsatira ndi kulemekeza m’pongozi wake, Naomi, mpaka mapeto, Mulungu anam'patsa m’dalitso wakukhala wophatikizika mu mbadwa za Israyeli.
Lero, mamembala a Mpingo wa Mulungu, monga Rute, amalemekeza makolo awo akuthupi komanso makolo awo auzimu, Atate Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, akukhala ndi moyo wokonzeka ndi madalitso a kumwamba.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi