Kunena, “Munthu amakolola zomwe wafesa,” Mulungu anatiphunzitsa kuti madalitso amabwereranso kwa ife pokhapokha titayankhura mawu a madalitso.
Khristu Ahnsahnghong anakhazikitsa Mpingo wa Mulungu ndi mwazi wamtengo wapatali wokhetsedwa pa mtanda Choncho mamembala a Ziyoni ayenera nthawi zonse kupereka ulemerero kwa Mulungu ndi kufesa mbewu za madalitso mwa anthu otizungulira ife ndi mawu achisomo.
Munthu wabwino atulutsa zabwino m’chuma chake chabwino, ndi munthu woipa atulutsa zoipa m’chuma chake choipa. Ndipo ndinena kwa inu, kuti mau onse opanda pake, amene anthu adzalankhula, adzawawerengera mlandu wake tsiku la kuweruza. Pakuti udzayesedwa wolungama ndi mau ako, ndipo ndi mau ako omwe udzatsutsidwa. Mateyu 12:35-37
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi